Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nalowa anawo, nalandira dzikoli likhale lao lao, ndipo munagonjetsa pamaso pao okhala m'dziko, ndiwo Akanani, ndi kuwapereka m'dzanja mwao, pamodzi ndi mafumu ao, ndi mitundu ya anthu ya m'dziko, kuti acite nao cifuniro cao.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:24 nkhani