Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngakhale apa atadzipangira mwana wa ng'ombe woyenga, nati, Suyu Mulungu wako anakukweza kucokera ku Aigupto, nacita zopeputsa zazikuru;

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:18 nkhani