Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nakana kumvera, osakumbukilansozodabwiza zanu munazicita pakati pao; koma anaumitsa khosi lao, ndipo m'kupanduka kwao anaika mtsogoleri abwerere kumka ku ukapolo wao; koma Inu ndinu Mulungu wokhululukira, wacisomo, ndi wansoni, wolekereza, ndi wocuruka cifundo; ndipo simunawasiya.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:17 nkhani