Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 8:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ezara mlembi anaima pa ciunda ca mitengo adacimangira msonkhanowo; ndi pambali: pace padaima Matitiya, ndi Sema, ndi Anaya, ndi Uriya, ndi Hilikiya, ndi Maaseya, ku dzanja lamanja lace; ndi ku dzanja lamanzere Pedaya, ndi Misayeli, ndi Malikiya, ndi Hasumu, ndi Hasibadana, Zekariya, ndi Mesulamu.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 8

Onani Nehemiya 8:4 nkhani