Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 8:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nawerenga m'menemo pa khwalala liri ku cipata ca kumadzi kuyambira mbanda kuca kufikira msana, pamaso pa amuna ndi akazi, ndi iwo okhoza kuzindikira; ndi anthu onse anacherera khutu buku la cilamulo.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 8

Onani Nehemiya 8:3 nkhani