Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 8:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanena naonso, Mukani mukadye zonona, mukamwe zozuna, nimumtumizire gawo lace iye amene sanamkonze ratu kanthu; cifukwa lero ndilo lopatulikira Ambuye wathu; ndipo musamacita cisoni; pakuti cimwemwe ca Yehova ndico mphamvu yanu.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 8

Onani Nehemiya 8:10 nkhani