Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 8:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu onse anasonkhana ngati munthu mmodzi ku khwalala liri ku cipata ca kumadzi, namuuza Ezara mlembi atenge buku la cilamulo ca Mose, cimene Yehova adalamulira Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 8

Onani Nehemiya 8:1 nkhani