Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 7:71 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Enanso a akuru a nyumba za makolo anapereka ku cuma ca nchitoyi, madariki agolidi zikwi makumi awiri, ndi miyeso ya siliva zikwi ziwiri mphambu mazana awiri.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 7

Onani Nehemiya 7:71 nkhani