Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 5:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinanena, nao, Ife monga umo tinakhoza, tinaombola abale athu Ayuda ogulitsidwa kwa amitundu; ndipo kodi inu mukuti mugulitse abale anu, kapena tiwagule ndi ife? Pamenepo anakhala du, nasowa ponena.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 5

Onani Nehemiya 5:8 nkhani