Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mtima wanga unandipangira; ndipo ndinatsutsana nao aufuru ndi olamulira, ndi kunena nao, Mukongoletsa mwa phindu yense kwa mbale wace. Ndipo ndinasonkhanitsa msonkhano waukuru wakuwatsutsa.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 5

Onani Nehemiya 5:7 nkhani