Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 4:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kuyambira pamenepo gawo lina la anyamata anga anagwira nchito, ndi gawo ina linagwira nthungo, zikopa, ndi mauta, ndi maraya acitsulo; ndi akuru anali m'mbuyo mwa nyumba yonse ya Yuda.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 4

Onani Nehemiya 4:16 nkhani