Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 4:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pakumva adani athu kuti cinadziwika nafe, ndi kuti Mulungu adapititsa pacabe uphungu wao, tinabwera tonse kumka kulinga, yense ku nchito yace.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 4

Onani Nehemiya 4:15 nkhani