Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 3:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi pambali pao anakonza Meremoti mwana wa Uliya, mwana wa Kozi. Ndi pambali pao anakonza Mesulamu mwana wa Berekiya, mwana wa Mesezabele. Ndi pambali pao anakonza Zadoki mwana wa Baana.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 3

Onani Nehemiya 3:4 nkhani