Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 12:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Aisrayeli onse m'masiku a Zerubabele, ndi m'masiku a Nehemiya, anapereka magawo a oyimbira ndi odikira, monga mudafunika tsiku ndi tsiku; nawapatulira Alevi; ndi Alevi anawapatulira ana a Aroni.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 12

Onani Nehemiya 12:47 nkhani