Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 12:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaphera nsembe zambiri tsiku lija, nasekerera; pakuti Mulungu anawakondweretsa ndi cimwemwe cacikuru; ndi akazi omwe ndi ana anakondwera; ndi cikondwerero ca Yerusalemu cinamveka kutali.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 12

Onani Nehemiya 12:43 nkhani