Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 12:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo popereka linga la Yerusalemu anafunafuna Alevi m'malo mwao monse, kubwera nao ku Yerusalemu, kuti acite kuperekaku mokondwera, ndi mayamiko, ndi kuyimbira, ndi nsanje, zisakasa, ndi azeze.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 12

Onani Nehemiya 12:27 nkhani