Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 10:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo mitundu ya anthu a m'dziko akabwera nao malonda, ngakhale tirigu, dzuwa la Sabata, kutsata malonda, sitidzagulana nao dzuwa la Sabata, kapena dzuwa lina lopatulika, ndi kuti tidzaleka caka cacisanu ndi ciwiri ndi mangawa ali onse.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 10

Onani Nehemiya 10:31 nkhani