Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 10:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amenewa anaumirira abale ao, omveka ao, nalowa m'temberero ndi lumbiro, kuti adzayenda m'cilamulo ca Mulungu anacipereka Mose mtumiki wa Mulungu, ndi kuti adzasunga ndi kucita zonse atilamulira Yehova Ambuye wathu, ndi maweruzo ace, ndi malemba ace;

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 10

Onani Nehemiya 10:29 nkhani