Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 10:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi anthu otsala, ansembe, Alevi, odikira, oyimbira, Anetini, ndi onse anadzisiyanitsawo pa mitundu ya anthu a m'dziko kutsata cilamulo ca Mulugu, akazi ao, ana ao amuna ndi akazi, yense wodziwa ndi wozindikira,

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 10

Onani Nehemiya 10:28 nkhani