Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 1:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova, mucherere khutu pemphero la kapolo wanu, ndi pemphero la akapolo anu okondwera nako kuopa dzina lanu; ndipo mulemereze kapolo wanu lero lino, ndi kumuonetsera cifundo pamaso pa munthu uyu. Koma ndinali ine wothirira mfumu cakumwa cace.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 1

Onani Nehemiya 1:11 nkhani