Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nahumu 2:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, nditsutsana nawe, ati Yehova wa makamu, ndipo ndidzatentha magareta ace m'utsi; ndi lupanga lidzadya misona yako ya mkango; ndipo ndidzacotsa zofunkha zako pa dziko lapansi, ndi mau a mithenga yako sadzamvekanso.

Werengani mutu wathunthu Nahumu 2

Onani Nahumu 2:13 nkhani