Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 9:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zonse zigwera onse cimodzimodzi; kanthu kamodzi kangogwera wolungama ndi woipa; ngakhale wabwino ndi woyera ndi wodetsedwa: ngakhale wopereka nsembe ndi wosapereka konse; wabwino alingana ndi wocimwa; wolumbira ndi woopa lumbiro.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 9

Onani Mlaliki 9:2 nkhani