Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 9:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti munthu sadziwatu mphindi yace; monga nsomba zigwidwa m'ukonde woipa, ndi mbalame zikodwa mumsampha, momwemo ana a anthu amagwidwa ndi nthawi ya tsoka, ngati msampha umene uwagwera modzidzimuka.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 9

Onani Mlaliki 9:12 nkhani