Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 9:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinabweranso ndi kuzindikira pansi pano kuti omwe atamanga msanga sapambana m'liwiro, ngakhale olimba sapambana m'nkhondo, ngakhale anzeru sapeza zakudya, ngakhale ozindikira bwino salemera, ngakhale odziwitsa sawakomera mtima; koma yense angoona zomgwera m'nthawi mwace.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 9

Onani Mlaliki 9:11 nkhani