Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 6:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

munthu amene Mulungu wamlemeretsa nampatsa cuma ndi ulemu, mtima wace susowa kanthu kena ka zonse azifuna, koma Mulungu osampatsa mphamvu ya kudyapo, koma mlendo adyazo; ici ndi cabe ndi nthenda yoipa,

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 6

Onani Mlaliki 6:2 nkhani