Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 6:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndani adziwa comwe ciri cabwino kwa munthu ali ndi moyo masiku onse a moyo wace wacabe umene autsiriza ngati mthunzi? pakuti ndani adzauza munthu cimene cidzaoneka m'tsogolo mwace kunja kuno?

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 6

Onani Mlaliki 6:12 nkhani