Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 4:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Awiri aposa mmodzi; pakuti ali ndi mphotho yabwino m'nchito zao.

10. Pakuti akagwa, wina adzautsa mnzace; koma tsoka wakugwa wopanda womnyamutsa.

11. Ndiponso awiri akagona limodzi afunditsana; koma mmodzi pa yekha kodi adzafunditsidwa bwanji?

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 4