Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 2:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti yemwe Mulungu amuyesa wabwino ampatsa nzeru ndi cidziwitso ndi cimwemwe; koma wocimwa amlawitsa bvuto la kusonkhanitsa ndi kukundika, kuti aperekere yemwe Mulungu amuyesa wabwino. Icinso ndi cabe ndi kungosautsa mtima.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 2

Onani Mlaliki 2:26 nkhani