Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mlaliki 2:25-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Pakuti ndani angadye ndi kufulumirako, koposa ine.

26. Pakuti yemwe Mulungu amuyesa wabwino ampatsa nzeru ndi cidziwitso ndi cimwemwe; koma wocimwa amlawitsa bvuto la kusonkhanitsa ndi kukundika, kuti aperekere yemwe Mulungu amuyesa wabwino. Icinso ndi cabe ndi kungosautsa mtima.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 2