Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 9:4-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Wacibwana yense apambukire kuno;Iti kwa yense wosowa nzeru,

5. Tiyeni, idyani cakudya canga;Nimumwe vinyo wanga ndamsanganiza.

6. Lekani, acibwana inu, nimukhale ndi moyo;Nimuyende m'njira ya nzeru.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 9