Ngwodala amene andimvera, nadikira pa zitseko zanga tsiku ndi tsiku,Ndi kulinda pa mphuthu za makoma anga;