Mnzako, ndi mnzace wa atate wako, usawasiye;Usanke ku nyumba ya mbale wako tsiku la tsoka lako;Mnansi wapafupi aposa mbale wakutari.