Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 2:14-17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Omwe asangalala pocita zoipa,Nakondwera ndi zokhota zoipa;

15. Amene apotoza njira zao,Nakhotetsa mayendedwe ao;

16. Nzeru idzakupulumutsa kwa mkazi waciwerewere,Kwa mkazi wacilendo wosyasyalika ndi mau ace;

17. Wosiya bwenzi la ubwana wace,Naiwala cipangano ca Mulungu wace;

Werengani mutu wathunthu Miyambi 2