Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 2:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mwananga, ukalandira mau anga,Ndi kusunga malamulo anga;

2. Kucherera makutu ako kunzeru,Kulozetsa mtima wako kukuzindikira;

3. Ukaitananso luntha,Ndi kupfuulira kuti ukazindikire;

4. Ukaifunafuna ngati siliva,Ndi kuipwaira ngati cuma cobisika;

Werengani mutu wathunthu Miyambi 2