Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 15:31-33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

31. Khutu lomvera cidzudzulo ca moyoLidzakhalabe mwa anzeru.

32. Wokana mwambo apeputsa moyo wace;Koma wosamalira cidzudzulo amatenga nzeru.

33. Kuopa Yehova ndiko mwambo wanzeru;Ndipo cifatso citsogolera ulemu.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 15