Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 15:13-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. Mtima wokondwa usekeretsa nkhope;Koma moyo umasweka ndi zowawa za m'mtima.

14. Mtima wa wozindikira ufunitsa kudziwa;Koma m'kamwa mwa opusa mudya utsiru.

15. Masiku onse a wosauka ali oipa;Koma wokondwera mtima ali ndi phwando losatha.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 15