Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 14:32-35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

32. Wocimwa adzakankhidwa m'kuipa kwace;Koma wolungama akhulupirirabe pomwalira,

33. Nzeru ikhalabe m'mtima wa wozindikira,Nidziwika pakati pa opusa.

34. Cilungamo cikuza mtundu wa anthu;Koma cimo licititsa pfuko manyazi.

35. Mfumu ikomera mtima kapolo wocita mwanzeru;Koma idzakwiyira wocititsa manyazi.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 14