Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 14:12-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Iripo njira yooneka kwa mwamuna ngati yoongoka;Koma matsiriziro ace ndi njira za imfa.

13. Ngakhale m'kuseka mtima uwawa;Ndipo matsiriziro a ciphwete ndi cisoni.

14. Wobwerera m'mbuyo m'mtima adzakhuta njira zace;Koma munthu wabwino adzakhuta za mwa iye yekha.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 14