Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 14:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mkazi yense wanzeru amanga banja lace;Koma wopusa alipasula ndi manja ace.

2. Woyenda moongoka mtima aopa Yehova;Koma wokhota m'njira yace amnyoza,

3. M'kamwa mwa citsiru muli ntyole ya kudzikuza;Koma milomo ya anzeru Idzawasunga.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 14