Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 13:16-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Yense wocenjera amacita mwanzeru:Koma wopusa aonetsa utsiru.

17. Mthenga wolakwa umagwa m'zoipa;Koma mtumiki wokhulupirika alamitsa.

18. Wokana mwambo adzasauka nanyozedwa;Koma wolabadira cidzudzulo adzalemekezedwa.

19. Cifuniro cikondweretsa moyo citacitidwa;Koma kusiya zoipa kunyansa opusa,

Werengani mutu wathunthu Miyambi 13