Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Miyambi 11:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Muyeso wonyenga unyansa Yehova;Koma mulingo wamphumphu umsekeretsa.

2. Pakudza kudzikuza padzanso manyazi;Koma nzeru iri ndi odzicepetsa,

3. Kuongoka mtima kwa olungama kuwatsogolera;Koma kukhota kwa aciwembu kudzawaononga.

Werengani mutu wathunthu Miyambi 11