Miyambi 1:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) MIYAMBI ya Solomo mwana wa Davide, mfumu ya Israyeli. Kudziwa nzeru ndi mwambo;Kuzindikira mau ozindikiritsa;