Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mika 7:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndani Mulungu wofanana ndi Inu, wakukhululukira mphulupulu, wakupitirira zolakwa za otsala a colowa cace? sasunga mkwiyo wace ku nthawi yonse popeza akondwera naco cifundo.

Werengani mutu wathunthu Mika 7

Onani Mika 7:18 nkhani