Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mika 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo otsala a Yakobo adzakhala pakati pa mitundu yambiri ya anthu, ngati mame ocokera kwa Yehova, ngati mvula paudzu, yosacedwera munthu, yosalindira ana a anthu.

Werengani mutu wathunthu Mika 5

Onani Mika 5:7 nkhani