Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mika 2:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akayenda ndi mtima wacinyengo ndi kunama, ndi kuti, Ndidzanenera kwa iwe za vinyo ndi cakumwa cakuledzeretsa; iye ndiye mneneri wa anthu ace.

Werengani mutu wathunthu Mika 2

Onani Mika 2:11 nkhani