Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mika 1:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa ca ici ndidzacita maliro, ndi kucema, ndidzayenda wolandidwa ndi wamarisece; ndidzalira ngati mimbulu, ndi kubuma ngati nthiwatiwa.

Werengani mutu wathunthu Mika 1

Onani Mika 1:8 nkhani