Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mika 1:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mafano ace osema onse adzaphwanyika, ndi mphotho zace zonse zidzatenthedwa ndi moto, ndi mafano ace onse ndidzawapasula; pakuti anazisonkhanitsa pa mphotho ya mkazi waciwerewere, ndipo zidzabwerera ku mphotho ya mkazi waciwerewere.

Werengani mutu wathunthu Mika 1

Onani Mika 1:7 nkhani