Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 96:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Myimbireni Yehova nyimbo yatsopano;Myimbireni Yehova, inu, dziko lonse lapansi.

2. Myimbireni Yehova, lemekezani dzina lace;Lalikirani cipulumutso cace tsiku ndi tsiku.

3. Fotokozerani ulemerero wace mwa amitundu;Zodabwiza zace mwa mitundu yonse ya anthu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 96