Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 92:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Nkokoma kuyamika Yehova,Ndi kuyimbira nyimbo dzina lanu, Wam'mwambamwamba Inu:

2. Kuonetsera cifundo canu mamawa,Ndi cikhulupiriko canu usiku uli wonse.

3. Pa coyimbira ca zingwe khumi ndi pacisakasa;Pazeze ndi kulira kwace.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 92