Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 90:16-17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Cocita Inu cioneke kwa atumiki anu,Ndi ulemerero wanu pa ana ao.

17. Ndipo cisomo cace ca Yehova Mulungu wathu cikhale pa ife;Ndipo mutikhazikitsire ife nchito ya manja athu;Inde, nchito ya manja athu muikhazikitse.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 90